Masalimo 17:5 - Buku Lopatulika M'mayendedwe anga ndasunga mabande anu, mapazi anga sanaterereke. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 M'mayendedwe anga ndasunga mabande anu, mapazi anga sanaterereke. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndayenda m'njira zanu nthaŵi zonse, sindidapatuke konse. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mayendedwe anga akhazikika pa njira zanu; mapazi anga sanaterereke. |
Inu Yehova, ndidziwa kuti njira ya munthu sili mwa iye mwini; sikuli kwa munthu woyenda kulongosola mapazi ake.
Adzasunga mapazi a okondedwa ake, koma oipawo adzawakhalitsa chete mumdima; pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu.