Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira.
Masalimo 17:11 - Buku Lopatulika Tsopano anatizinga m'mayendedwe athu, apenyetsetsa m'maso kuti atigwetse pansi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tsopano anatizinga m'mayendedwe athu, apenyetsetsa m'maso kuti atigwetse pansi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amangondilondola ndi kundizinga. Amandiyang'ana kuti apeze njira yondigwetsera pansi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Andisaka, tsopano andizungulira ndi maso awo atcheru, kuti andigwetse pansi. |
Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira.
Ndipo Saulo anamuka mbali ina ya phiri, Davide ndi anthu ake kuseri kwake; ndipo Davide anafulumira kuthawa, chifukwa cha kuopa Saulo; popeza Saulo ndi anthu ake anazinga Davide ndi anthu ake kwete kuti awagwire.