Masalimo 144:3 - Buku Lopatulika Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yehova, munthu ndani kuti mumdziwa? Mwana wa munthu kuti mumsamalira? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Chauta, kodi munthu nchiyani, kuti muzimsamala? Mwana wa munthu nchiyani, kuti muzimganizira? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Inu Yehova, munthu nʼchiyani kuti mumamusamalira, mwana wa munthu kuti muzimuganizira? |
Siyani munthu, amene mpweya wake uli m'mphuno mwake; chifukwa m'mene awerengedwamo ndi muti?
Koma wina anachita umboni pena, nati, Munthu nchiyani kuti mumkumbukira iye? Kapena mwana wa munthu kuti mucheza naye?