Masalimo 140:11 - Buku Lopatulika Munthu wamlomo sadzakhazikika padziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Munthu wamlomo sadzakhazikika pa dziko lapansi; choipa chidzamsaka munthu wachiwawa kuti chimgwetse. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Musalole kuti woononga mbiri ya mnzake akhazikike m'dziko. Choipa chimlondole munthu wankhanza mpaka kumuwononga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Musalole kuti anthu achipongwe akhazikike mʼdziko; choyipa chilondole anthu ankhanza. |
Tsoka kwa woipa! Kudzamuipira; chifukwa kuti mphotho ya manja ake idzapatsidwa kwa iye.