Masalimo 139:5 - Buku Lopatulika Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, nimunaika dzanja lanu pa ine. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Munandizinga kumbuyo ndi kumaso, nimunaika dzanja lanu pa ine. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo, ndipo mumandisanjika dzanja lanu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mumandizinga kumbuyo ndi kutsogolo komwe; mwasanjika dzanja lanu pa ine. |
Koma sanatulutse dzanja lake pa akulu a ena a Israele; ndipo anapenya Mulungu, nadya, namwa.
Mulungu wamuyaya ndiye mokhaliramo mwako; ndi pansipo pali manja osatha. Ndipo aingitsa mdani pamaso pako, nati, Ononga.
Ndipo pamene ndinamuona Iye, ndinagwa pa mapazi ake ngati wakufa; ndipo anaika dzanja lake lamanja pa ine, nati, Usaope, Ine ndine Woyamba ndi Wotsiriza,