Munthu akadza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sangathe kukhala wophunzira wanga.
Masalimo 139:22 - Buku Lopatulika Ndidana nao ndi udani weniweni, ndiwayesa adani. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndidana nao ndi udani weniweni, ndiwayesa adani. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndimadana nawo ndi chidani chenicheni. Ndimaŵayesa adani anga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndimadana nawo kwathunthu; ndi adani anga. |
Munthu akadza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sangathe kukhala wophunzira wanga.