Atsitsimutsa moyo wanga; anditsogolera m'mabande a chilungamo, chifukwa cha dzina lake.
Masalimo 139:10 - Buku Lopatulika kungakhale komweko dzanja lanu lidzanditsogolera, nilidzandigwira dzanja lanu lamanja. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kungakhale komweko dzanja lanu lidzanditsogolera, nilidzandigwira dzanja lanu lamanja. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ngakhale kumenekonso mudzanditsogolera, dzanja lanu lamanja lidzandichirikiza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kumenekonso dzanja lanu lidzanditsogolera, dzanja lanu lamanja lidzandigwiriziza. |
Atsitsimutsa moyo wanga; anditsogolera m'mabande a chilungamo, chifukwa cha dzina lake.
Pakuti Ine Yehova Mulungu wako ndidzagwira dzanja lako lamanja, ndi kunena kwa iwe, Usaope ndidzakuthandiza iwe.
Angakhale abisala pamwamba pa Karimele, ndidzawapwaira ndi kuwatenga komweko; angakhale abisala pamaso panga pansi pa nyanja, kumeneko ndidzalamulira njoka, ndipo idzawaluma.