Masalimo 136:7 - Buku Lopatulika Amene analenga miuni yaikulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Amene analenga miuni yaikulu; pakuti chifundo chake nchosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adalenga miyuni yaikulu yamumlengalenga, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amene anapanga miyuni ikuluikulu, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. |
ndi kuti mungakweze maso anu kupenya kumwamba, ndipo poona dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la kumwamba, munganyengedwe ndi kuzigwadira, ndi kuzitumikira, zimene Yehova Mulungu wanu anagawira mitundu yonse ya anthu pansi pa thambo lonse.