Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.
Masalimo 136:25 - Buku Lopatulika Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Amapatsa zamoyo zonse chakudya, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amene amapereka chakudya kwa cholengedwa chilichonse, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. |
Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.