Masalimo 136:21 - Buku Lopatulika Ndipo anapereka dziko lao likhale cholowa; pakuti chifundo chake nchosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anapereka dziko lao likhale chosiyira; pakuti chifundo chake nchosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Napereka dziko la mafumuwo kuti likhale choloŵa, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Napereka dziko lawo ngati cholowa, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. |
Ndipo anapirikitsa amitundu pamaso pao, nawagawira cholowa chao, ndi muyeso, nakhalitsa mafuko a Israele m'mahema mwao.
Koma iwe, Israele, mtumiki wanga, Yakobo, amene ndinakusankha, mbeu ya Abrahamu bwenzi langa;
Ndipo ndinauza inu muja, ndi kuti, Yehova Mulungu wanu wakupatsani dziko ili likhale lanulanu, muoloke, amuna onse amphamvu ovala zida zao, pamaso pa abale anu ana a Israele.