Ndipo anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo inaphwa: Potero anawayendetsa mozama ngati m'chipululu.
Masalimo 136:14 - Buku Lopatulika Napititsa Israele pakati pake; pakuti chifundo chake nchosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Napititsa Israele pakati pake; pakuti chifundo chake nchosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaolotsa Aisraele pakati pake, pakuti chikondi chake nchamuyaya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nadutsitsa Israeli pakati pa nyanjayo, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. |
Ndipo anadzudzula Nyanja Yofiira, ndipo inaphwa: Potero anawayendetsa mozama ngati m'chipululu.
Ndipo ana a Israele analowa pakati pa nyanja pouma; ndi madziwo anakhala kwa iwo ngati khoma palamanja, ndi palamanzere.