Ndipo anaika chakudya pamaso pake: koma anati, Sindidzadya ndisananene chimene ndadzera. Ndipo anati, Nenatu.
Masalimo 132:4 - Buku Lopatulika ngati ndidzalola maso anga agone, kapena zikope zanga ziodzere; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ngati ndidzalola maso anga agone, kapena zikope zanga ziodzere; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa sindidzalola kuti ndikhale m'tulo kapena kuti zikope zanga ziwodzere, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero sindidzalola kuti maso anga agone, kapena zikope zanga ziwodzere, |
Ndipo anaika chakudya pamaso pake: koma anati, Sindidzadya ndisananene chimene ndadzera. Ndipo anati, Nenatu.
Ndipo anati, Khala ulipo, mwana wanga, mpaka udziwa umo ukhalire mlandu; pakuti munthuyo sadzauleka mpaka atautha mlanduwo lero lino.