Masalimo 131:3 - Buku Lopatulika Israele, uyembekezere Yehova, kuyambira tsopano kufikira kosatha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Israele, uyembekezere Yehova, kuyambira tsopano kufikira kosatha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iwe Israele, khulupirira Chauta kuyambira tsopano mpaka muyaya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yembekeza Yehova, iwe Israeli, kuyambira tsopano mpaka muyaya. |
Yehova adzasungira kutuluka kwako ndi kulowa kwako, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.
Israele, uyembekezere Yehova; chifukwa kwa Yehova kuli chifundo, kwaonso kuchulukira chiombolo.
Wodala munthu amene akhala naye Mulungu wa Yakobo kuti amthandize, chiyembekezo chake chili pa Yehova, Mulungu wake.
Khulupirirani Yehova nthawi zamuyaya, pakuti mwa Ambuye Yehova muli thanthwe lachikhalire.