Akadapanda kukhala nafe Yehova, pakutiukira anthu:
Chauta akadapanda kukhala pa mbali yathu, pamene anthu adatiwukira,
akanapanda kukhala mbali yathu Yehova, potiwukira anthuwo,
Pakuti andizinga agalu, msonkhano wa oipa wanditsekereza; andiboola m'manja anga ndi m'mapazi anga.
Yehova! Ha! Achuluka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri.
Ambiri amati kwa moyo wanga, alibe chipulumutso mwa Mulungu.
Woipa aunguza wolungama, nafuna kumupha.
Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ake, mwa Yehova ndidzalemekeza mau ake.