Ine ndine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika mu Israele; inu mulikufuna kuononga mzinda ndi mai wa mu Israele; mudzamezeranji cholowa cha Yehova?
Masalimo 120:7 - Buku Lopatulika Ine ndikuti, Mtendere; koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ine ndikuti, Mtendere; koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ine ndimafuna mtendere, koma ndikalankhula za mtendere, iwo amafuna nkhondo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ine ndine munthu wamtendere; koma ndikamayankhula, iwo amafuna nkhondo. |
Ine ndine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika mu Israele; inu mulikufuna kuononga mzinda ndi mai wa mu Israele; mudzamezeranji cholowa cha Yehova?
Londolani mtendere ndi anthu onse, ndi chiyeretso chimene, akapanda ichi, palibe mmodzi adzaona Ambuye: