ndi mkwiyo wanga udzayaka, ndipo ndidzapha inu ndi lupanga; ndipo akazi anu adzakhala amasiye, ndi ana anu omwe.
Masalimo 109:9 - Buku Lopatulika Ana ake akhale amasiye, ndi mkazi wake wamasiye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana ake akhale amasiye, ndi mkazi wake wamasiye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ana ake akhale amasiye, ndipo mkazi wake akhale mfedwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ana ake akhale amasiye ndipo mkazi wake akhale wopanda mwamuna. |
ndi mkwiyo wanga udzayaka, ndipo ndidzapha inu ndi lupanga; ndipo akazi anu adzakhala amasiye, ndi ana anu omwe.
Chifukwa chake mupereke ana ao kunjala, mupereke iwo kumphamvu ya lupanga; akazi ao akhale opanda ana, ndi amasiye; amuna ao aphedwe ndi imfa, ndi anyamata ao apandidwe ndi lupanga kunkhondo.