Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira kudzenje la chionongeko. Anthu okhetsa mwazi ndi achinyengo masiku ao sadzafikira nusu; koma ine ndidzakhulupirira Inu.
Masalimo 109:8 - Buku Lopatulika Masiku ake akhale owerengeka; wina alandire udindo wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Masiku ake akhale owerengeka; wina alandire udindo wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Masiku ake akhale oŵerengeka, wina alandire udindo wake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Masiku ake akhale owerengeka; munthu wina atenge malo ake a utsogoleri. |
Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira kudzenje la chionongeko. Anthu okhetsa mwazi ndi achinyengo masiku ao sadzafikira nusu; koma ine ndidzakhulupirira Inu.