Chimene adagwiriracho ntchito, adzachibweza, osachimeza; sadzakondwera monga mwa zolemera zake adaziona.
Masalimo 109:11 - Buku Lopatulika Wokongoletsa agwire zonse ali nazo; ndi alendo alande za ntchito yake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wokongoletsa agwire zonse ali nazo; ndi alendo alande za ntchito yake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Wokongoza ndalama amlande zonse zimene ali nazo. Alendo afunkhe zimene adapindula ndi ntchito yake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Wokongoza alande zonse zimene ali nazo; alendo afunkhe ntchito za manja ake. |
Chimene adagwiriracho ntchito, adzachibweza, osachimeza; sadzakondwera monga mwa zolemera zake adaziona.
ndipo mudzafufuza usana, monga wakhungu amafufuza mumdima, ndipo simudzapindula nazo njira zanu; koma mudzakhala wopsinjika, nadzakuberani masiku onse, wopanda wina wakukupulumutsani.