Lemekezani Yehova, inu, ntchito zake zonse, ponseponse pali ufumu wake: Lemekeza Yehova, moyo wanga iwe.
Masalimo 108:2 - Buku Lopatulika Galamukani, chisakasa ndi zeze; ndidzauka ndekha mamawa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Galamukani, chisakasa ndi zeze; ndidzauka ndekha mamawa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu zeze ndi pangwe, tiyeni lirani. Ndidzadzutsa dzuŵa ndi nyimbo zanga. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Dzukani, zeze ndi pangwe! Ine ndidzadzutsa mʼbandakucha. |
Lemekezani Yehova, inu, ntchito zake zonse, ponseponse pali ufumu wake: Lemekeza Yehova, moyo wanga iwe.
Galamuka, Debora, galamuka, galamuka, galamuka, unene nyimbo; uka, Baraki, manga nsinga ndende zako, mwana wa Abinowamu, iwe.