Ndipo madzi analinkuchepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri.
Masalimo 104:8 - Buku Lopatulika anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, kufikira malo mudawakonzeratu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, kufikira malo mudawakonzeratu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mapiri adatumphuka, zigwa zidatsika, mpaka kumene Inu mudaakonzeratu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Inu munamiza mapiri, iwo anatsikira ku zigwa kumalo kumene munawakonzera. |
Ndipo madzi analinkuchepa kufikira mwezi wakhumi; mwezi wakhumi tsiku loyamba mwezi ndipo padaoneka mitu ya mapiri.