Zimamwamo nyama zonse zakuthengo; mbidzi zipherako ludzu lao.
Zimamwamo nyama zonse za kuthengo; mbidzi zipherako ludzu lao.
Imapatsa nyama zonse zakuthengo madzi akumwa, mbidzi zimapherapo ludzu.
Iwo amapereka madzi kwa zirombo zonse zakuthengo; abulu akuthengo amapha ludzu lawo.
Iye amwetsa mapiri mochokera m'zipinda zake: Dziko lakhuta zipatso za ntchito zanu.
Muolowetsa dzanja lanu, nimukwaniritsira zamoyo zonse chokhumba chao.