Ndipo Afarisi anatuluka, nayamba kufunsana naye, ndi kufuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba, namuyesa Iye.
Marko 9:16 - Buku Lopatulika Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsana nao chiyani? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anawafunsa iwo, Mufunsana nao chiyani? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iye adaŵafunsa kuti, “Kodi mukutsutsana zotani?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anafunsa kuti, “Mukukangana nawo chiyani iwowa?” |
Ndipo Afarisi anatuluka, nayamba kufunsana naye, ndi kufuna kwa Iye chizindikiro chochokera Kumwamba, namuyesa Iye.
Ndipo pomwepo anthu onse a khamulo, pakumuona Iye, anazizwa kwambiri, namthamangira Iye, namlonjera.
Ndipo wina wa m'khamulo anamyankha Iye, kuti, Mphunzitsi, ndadza naye kwa Inu mwana wanga, ali nao mzimu wosalankhula;