Marko 8:10 - Buku Lopatulika Ndipo pomwepo analowa m'ngalawa ndi ophunzira ake, nafika ku mbali ya ku Dalamanuta. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pomwepo analowa m'ngalawa ndi ophunzira ake, nafika ku mbali ya ku Dalamanuta. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake Yesu adatsazikana nawo anthu aja, kenaka Iye ndi ophunzira ake adaloŵa m'chombo napita ku dera la Dalamanuta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero analowa mʼbwato pamodzi ndi ophunzira ake napita ku dera la Dalamanuta. |