koma inu munena, Munthu akati kwa atate wake, kapena amai wake, Korban, ndiko kuti Mtulo, chimene ukadathandizidwa nacho ndi ine,
Marko 7:12 - Buku Lopatulika simulolanso kumchitira kanthu atate wake kapena amai wake; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 simulolanso kumchitira kanthu atate wake kapena amai wake; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ameneyo sasoŵanso kuŵathandiza atate ake ndi amai ake.’ Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero pamenepo inu simumalola kuti achitire kanthu kalikonse abambo kapena amayi ake. |
koma inu munena, Munthu akati kwa atate wake, kapena amai wake, Korban, ndiko kuti Mtulo, chimene ukadathandizidwa nacho ndi ine,
muyesa achabe mau a Mulungu mwa mwambo wanu, umene munaupereka: ndi zinthu zotere zambiri muzichita.