Ndipo pamalo ponse sakulandirani, kapena kumvera inu, pakuchoka kumeneko, sansani fumbi lili kumapazi anu, likhale mboni ya kwa iwo.
Marko 6:10 - Buku Lopatulika Ndipo ananena nao, Kumene kulikonse mukalowa m'nyumba, khalani komweko kufikira mukachokako. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ananena nao, Kumene kulikonse mukalowa m'nyumba, khalani komweko kufikira mukachokako. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaŵauzanso kuti, “Mukafika pa mudzi, muzikhala nao kunyumba kumene mudafikirako, mpaka itakwana nthaŵi yoti muchoke kumudziko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene mulowa mʼnyumba mukakhale momwemo kufikira mutachoka mʼmudzimo. |
Ndipo pamalo ponse sakulandirani, kapena kumvera inu, pakuchoka kumeneko, sansani fumbi lili kumapazi anu, likhale mboni ya kwa iwo.
Pamene anabatizidwa iye ndi a pabanja pake anatidandaulira ife, kuti, Ngati mwandiyesera ine wokhulupirika kwa Ambuye, mulowe m'nyumba yanga, mugone m'menemo. Ndipo anatiumiriza ife.