Ndipo m'kufesa kwake zina zinagwa m'mbali mwa njira, ndipo zinadza mbalame, nkulusira izo.
Marko 6:1 - Buku Lopatulika Ndipo Iye anatuluka kumeneko; nafika kudziko la kwao; ndipo ophunzira ake anamtsata. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Iye anatuluka kumeneko; nafika kudziko la kwao; ndipo ophunzira ake anamtsata. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adachoka kumeneko, nakafika kumudzi kwao. Ophunzira ake adatsagana naye. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anachoka kumeneko napita ku mudzi kwawo, pamodzi ndi ophunzira ake. |
Ndipo m'kufesa kwake zina zinagwa m'mbali mwa njira, ndipo zinadza mbalame, nkulusira izo.
nadza nakhazikika m'mzinda dzina lake Nazarete kuti chikachitidwe chonenedwa ndi aneneri kuti, Adzatchedwa Mnazarayo.
Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Mneneri sakhala wopanda ulemu, koma m'dziko la kwao ndimo, ndi pakati pa abale ake, ndi m'nyumba yake.