Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Belezebulu, ndipo, Ndi mkulu wao wa ziwanda atulutsa ziwanda.
Marko 5:10 - Buku Lopatulika Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo iye adadandaulira Yesu kwambiri kuti mizimuyo asaitulutsire kunja kwa dera limenelo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo anamupempha Yesu mobwerezabwereza kuti asazitulutse mʼderalo. |
Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Belezebulu, ndipo, Ndi mkulu wao wa ziwanda atulutsa ziwanda.
Ndipo anailola. Ndipo mizimu yonyansa inatuluka, nilowa mu nkhumba; ndipo gulu linatsika liwiro potsetsereka ndi kulowa m'nyanja, ndizo ngati zikwi ziwiri; ndipo zinatsamwa m'nyanja.
Ndipo anamfunsa, Dzina lako ndani? Ndipo ananena kwa Iye, Dzina langa ndine Legio; chifukwa tili ambiri.