Pomwepo Yesu ananena kwa iye, Choka Satana, pakuti kwalembedwa, Ambuye Mulungu wako udzamgwadira, ndipo Iye yekhayekha udzamlambira.
Marko 3:26 - Buku Lopatulika Ndipo Satana akadziukira mwini yekha, nagawanika, sangathe kukhazikika, koma atsirizika. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Satana akadziukira mwini yekha, nagawanika, sakhoza kukhazikika, koma atsirizika. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ngati a mu ufumu wa Satana aukirana okhaokha nagaŵikana, Satanayo sangalimbe, ndiye kuti watha basi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ngati Satana adzitsutsa yekha sangathe kuyima; ulamuliro wake watha. |
Pomwepo Yesu ananena kwa iye, Choka Satana, pakuti kwalembedwa, Ambuye Mulungu wako udzamgwadira, ndipo Iye yekhayekha udzamlambira.