Ndipo abale ake anaona kuti atate wake anamkonda iye koposa abale ake onse: ndipo anamuda iye, ndipo sanathe kulankhula ndi iye mwamtendere.
Marko 3:25 - Buku Lopatulika Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, singathe kukhazikika nyumbayo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, sikhoza kukhazikika nyumbayo, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo anthu a m'banja limodzi akayamba kugaŵikana, banja lotere silingalimbe. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngati nyumba igawanikana mwa iyo yokha, nyumba imeneyo singathe kuyima. |
Ndipo abale ake anaona kuti atate wake anamkonda iye koposa abale ake onse: ndipo anamuda iye, ndipo sanathe kulankhula ndi iye mwamtendere.
Ndipo Satana akadziukira mwini yekha, nagawanika, sangathe kukhazikika, koma atsirizika.
Pakuti pomwe pali kaduka ndi zotetana, pamenepo pali chisokonekero ndi chochita choipa chilichonse.