Marko 16:2 - Buku Lopatulika Ndipo anadza kumanda mamawa tsiku loyamba la Sabata, litatuluka dzuwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anadza kumanda mamawa tsiku loyamba la Sabata, litatuluka dzuwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'mamaŵa ndithu pa tsiku lotsatira Sabatayo, adapita kumanda kuja, dzuŵa litatuluka. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mmamawa, tsiku loyamba la Sabata, dzuwa litangotuluka kumene, anali pa ulendo wopita ku manda |
Ndipo popita tsiku la Sabata, mbandakucha, tsiku lakuyamba la sabata, anadza Maria wa Magadala, ndi Maria winayo, kudzaona manda.
Ndipo litapita Sabata, Maria wa Magadala, ndi Maria amake wa Yakobo, ndi Salome, anagula zonunkhira, kuti akadze kumdzoza Iye.
Koma tsiku loyamba la sabata, mbandakucha, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza.
Koma tsiku loyamba la Sabata anadza Maria wa Magadala mamawa, kusanayambe kucha, kumanda, napenya mwala wochotsedwa kumanda.