Marko 15:9 - Buku Lopatulika Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pilato adaŵafunsa kuti, “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayudayi?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda?” Pilato anafunsa, |
Ndipo khamu la anthu anabwera nayamba kupempha kuti achite monga anali kuwachitira nthawi zonse.
Koma muli nao makhalidwe, akuti ndimamasulira inu mmodzi pa Paska; kodi mufuna tsono kuti ndimasulire inu mfumu ya Ayuda?