Mudziwa kuti akapita masiku awiri, Paska afika, ndipo Mwana wa Munthu adzaperekedwa kupachikidwa pamtanda.
Marko 15:6 - Buku Lopatulika Ndipo ankawamasulira pachikondwerero wandende mmodzi, amene iwo anampempha. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ankawamasulira pachikondwerero wandende mmodzi, amene iwo anampempha. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pa nthaŵi ya chikondwerero cha Paska, bwanamkubwa ankaŵamasulira mkaidi mmodzi, yemwe Ayudawo ankapempha. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa nthawi ya Phwando, panali chizolowezi chomasula munthu wamʼndende amene anthu amupempha. |
Mudziwa kuti akapita masiku awiri, Paska afika, ndipo Mwana wa Munthu adzaperekedwa kupachikidwa pamtanda.
Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, womangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumpanduko.
koma Petro anaima kukhomo kunja. Chifukwa chake wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anatuluka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.
Koma zitapita zaka ziwiri Porkio Fesito analowa m'malo a Felikisi; ndipo Felikisi pofuna kukonda Ayuda anamsiya Paulo m'nsinga.
Koma Fesito pofuna kuyesedwa wachisomo ndi Ayuda, anayankha kwa Paulo, nati, Kodi ufuna kukwera kunka ku Yerusalemu, ndi kuweruzidwa ndi ine pomwepo kunena za zinthu izi?