Koma ophunzira khumi ndi mmodziwo anamuka ku Galileya, kuphiri kumene Yesu anawapangira.
Marko 15:41 - Buku Lopatulika amene anamtsata Iye, pamene anali mu Galileya, namtumikira; ndi akazi ena ambiri, amene anakwera kudza ndi Iye ku Yerusalemu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 amene anamtsata Iye, pamene anali m'Galileya, namtumikira; ndi akazi ena ambiri, amene anakwera kudza ndi Iye ku Yerusalemu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Azimaiŵa ankatsata Yesu pamene Iye anali ku Galileya, ndi kumamtumikira. Padaalinso azimai ena ambiri omwe adaabwera naye ku Yerusalemuko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amayi awa ankamutsatira Iye mu Galileya ndi kumutumikira Iye pa zosowa zake. Amayi enanso ambiri amene anabwera naye ku Yerusalemu analinso pomwepo. |
Koma ophunzira khumi ndi mmodziwo anamuka ku Galileya, kuphiri kumene Yesu anawapangira.