Ndipo Pilato anawayankhanso, nati kwa iwo, Pamenepo ndidzachita chiyani ndi Iye amene mumtchula mfumu ya Ayuda?
Marko 15:13 - Buku Lopatulika Ndipo anafuulanso, Mpachikeni pamtanda. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anafuulanso, Mpachikeni pamtanda. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthuwo adafuula kuti, “Mpachikeni pa mtanda!” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anafuwula kuti, “Mpachikeni!” |
Ndipo Pilato anawayankhanso, nati kwa iwo, Pamenepo ndidzachita chiyani ndi Iye amene mumtchula mfumu ya Ayuda?
Ndipo Pilato ananena nao, Pakuti Iye anachita choipa chotani? Koma iwo anafuulitsatu, Mpachikeni Iye.