Masiku ao Yehova anayamba kusadza Israele; ndipo Hazaele anawakantha m'malire onse a Israele,
Marko 14:71 - Buku Lopatulika Koma iye anayamba kutemberera, ndi kulumbira, Sindimdziwa munthuyu mulikunena. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma iye anayamba kutemberera, ndi kulumbira, Sindimdziwa munthuyu mulikunena. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma Petro adayamba kudzitemberera nkumalumbira kuti, “Mtheradi, munthu amene mukunenayu ine sindimdziŵa.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye anayamba kudzitemberera, nalumbira kuti, “Sindimudziwa munthu ameneyu.” |
Masiku ao Yehova anayamba kusadza Israele; ndipo Hazaele anawakantha m'malire onse a Israele,
Koma anakananso. Ndipo patapita kamphindi, akuimirirapo ananenanso ndi Petro, Zedi uli wa awo; pakutinso uli Mgalileya.
Ndipo pomwepo tambala analira kachiwiri. Ndipo Petro anakumbukira umo Yesu anati kwa iye, kuti, Tambala asanalire kawiri udzandikana katatu. Ndipo pakuganizira ichi analira misozi.