Marko 13:18 - Buku Lopatulika Ndipo pempherani kuti kusakhale m'nyengo yachisanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pempherani kuti kusakhale m'nyengo yachisanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pempherani kuti zimenezi zisadzaoneke pa nyengo yachisanu, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pempherani kuti zimenezi zisadzachitike nthawi yozizira, |
Pakuti masiku aja padzakhala chisautso, chonga sichinakhala chinzake kuyambira chiyambi cha chilengedwe chimene Mulungu anachilenga ndi kufikira tsopano, ndipo sichidzakhalanso, nthawi zonse.