ndi iye amene ali pamwamba pa tsindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake;
Marko 13:16 - Buku Lopatulika ndi iye amene ali kumunda asabwere kudzatenga malaya ake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi iye amene ali kumunda asabwere kudzatenga malaya ake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yemwe ali ku munda, asabwererenso ku nyumba kuti akatenge mwinjiro. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Aliyense amene ali ku munda asabwerere kukatenga mkanjo wake. |
ndi iye amene ali pamwamba pa tsindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake;