Mverani fanizo lina: Panali munthu, mwini banja, amene analima munda wampesa, nauzunguniza linga, nakumba umo moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.
Marko 12:8 - Buku Lopatulika Ndipo anamtenga, namupha iye, namtaya kunja kwa munda. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anamtenga, namupha iye, namtaya kunja kwa munda. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono adamugwiradi, namupha nkumuponya kunja kwa mundawo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo anamutenga ndi kumupha, ndipo anamuponya kunja kwa munda wamphesa. |
Mverani fanizo lina: Panali munthu, mwini banja, amene analima munda wampesa, nauzunguniza linga, nakumba umo moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina.
Koma olima ajawo, ananena mwa iwo okha, Ameneyu ndiye wolowa nyumba; tiyeni timuphe iye, ndipo mundawu udzakhala wathu.
Pamenepo mwini munda adzachita chiyani? Adzafika, nadzaononga olimawo, nadzapereka mundawo kwa ena.
Ndipo anamponya kunja kwa mundawo, namupha. Pamenepo mwini munda wampesawo adzawachitira chiyani?