Marko 11:6 - Buku Lopatulika Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ophunzirawo adaŵayankha monga momwe adaaŵauzira Yesu. Tsono anthuwo adaŵalola kuti ammasule. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo anayankha monga mmene Yesu anawawuzira, ndipo anthu aja anawalola kuti apite. |
Ndipo anabwera naye mwana wa bulu kwa Yesu, naika zovala zao pa iye, ndipo Iye anakhala pamenepo.