nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.
Marko 11:5 - Buku Lopatulika Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Muchita chiyani ndi kumasula mwana wa bulu? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Muchita chiyani ndi kumasula mwana wa bulu? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu amene adaali pamenepo adaŵafunsa kuti, “Inu nchiyani chimenecho, buluyo mukummasuliranji?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero anthu ena amene anayima pomwepo anafunsa kuti, “Mukuchita chiyani, kumasula mwana wabuluyo?” |
nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.
Ndipo anachoka, napeza mwana wa bulu womangidwa pakhomo, pabwalo m'khwalala, nammasula iye.