Chifukwa chake chimene Mulungu anachimanga pamodzi, asachilekanitse munthu.
Tsono zimene Mulungu wazilumikiza pamodzi, munthu asazilekanitse.”
Chifukwa chake chimene Mulungu wachilumikiza pamodzi, munthu wina asachilekanitse.”
Ndipo m'nyumba ophunzira anamfunsanso za chinthu ichi.
ndipo awiriwa adzakhala thupi limodzi: kotero kuti salinso awiri, koma thupi limodzi.