Iye adzadyetsa zoweta zake ngati mbusa, nadzasonkhanitsa anaankhosa m'manja mwake, nadzawatengera pa chifuwa chake, ndipo adzatsogolera bwinobwino zimene ziyamwitsa.
Marko 10:16 - Buku Lopatulika Ndipo Iye anatiyangata, natidalitsa, ndi kuika manja ake pa ito. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Iye anatiyangata, natidalitsa, ndi kuika manja ake pa ito. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Atatero adayamba kuŵafungata anawo, naŵasanjika manja ndi kuŵadalitsa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo ananyamula ana mʼmanja ake, ndi kuyika manja ake pa iwo nawadalitsa. |
Iye adzadyetsa zoweta zake ngati mbusa, nadzasonkhanitsa anaankhosa m'manja mwake, nadzawatengera pa chifuwa chake, ndipo adzatsogolera bwinobwino zimene ziyamwitsa.
Ndipo pamene iwo analikudya, Iye anatenga mkate, ndipo pamene anadalitsa, ananyema, napereka kwa iwo, kuti, Tengani; thupi langa ndi ili.