sonkhanitsani anthu, patulani msonkhano, memezani akuluakulu, sonkhanitsani ana ndi oyamwa mawere; mkwati atuluke m'chipinda mwake, ndi mkwatibwi m'mogona mwake.
Marko 10:13 - Buku Lopatulika Ndipo analinkudza nato kwa Iye tiana, kuti akatikhudze; ndipo ophunzirawo anawadzudzula. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo analinkudza nato kwa Iye tiana, kuti akatikhudze; ndipo ophunzirawo anawadzudzula. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu ena ankabwera ndi ana kwa Yesu kuti aŵakhudze ndi kuŵadalitsa, ophunzira ake nkumaŵazazira. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anthu anabweretsa ana kwa Yesu kuti awadalitse, koma ophunzira anawadzudzula. |
sonkhanitsani anthu, patulani msonkhano, memezani akuluakulu, sonkhanitsani ana ndi oyamwa mawere; mkwati atuluke m'chipinda mwake, ndi mkwatibwi m'mogona mwake.
Ndipo ambiri anamulamula kuti atonthole: koma makamaka anafuulitsa kuti, Inu mwana wa Davide, mundichitire chifundo.
Yohane anati kwa Iye, Mphunzitsi, tinaona munthu alikutulutsa ziwanda m'dzina lanu; ndipo tinamletsa, chifukwa sanalikutsata ife.