Malaki 2:3 - Buku Lopatulika
Taonani, ndidzaipsa mbeu chifukwa cha inu, ndi kuwaza ndowe pankhope panu, ndizo ndowe za nsembe zanu, ndipo adzakuchotsani pamodzi nacho.
Onani mutuwo
Taonani, ndidzaipsa mbeu chifukwa cha inu, ndi kuwaza ndowe pankhope panu, ndizo ndowe za nsembe zanu, ndipo adzakuchotsani pamodzi nacho.
Onani mutuwo
“Ndidzalanga zidzukulu zanu. Ndidzakupakani ndoŵe za nsembe zanu kumaso, ndipo ndidzakutayani ku nkhuti ya ndoŵe.
Onani mutuwo
“Ine ndidzalanga zidzukulu zanu chifukwa cha inu; ndidzakupakani kumaso ndowe za nsembe zanu zachikondwerero, ndipo ndidzakutayani pamodzi ndi ndowezo.”
Onani mutuwo