Chifukwa chake pamene Asamariya anadza kwa Iye, anamfunsa akhale nao; ndipo anakhala komweko masiku awiri.
Machitidwe a Atumwi 8:8 - Buku Lopatulika Ndipo panakhala chimwemwe chachikulu m'mzindamo. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo panakhala chimwemwe chachikulu m'mudzimo. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Choncho munali chimwemwe chachikulu mumzinda muja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kotero munali chimwemwe chachikulu mu mzindawo. |
Chifukwa chake pamene Asamariya anadza kwa Iye, anamfunsa akhale nao; ndipo anakhala komweko masiku awiri.
Ndipo pakumva ichi amitundu anakondwera, nalemekeza mau a Mulungu; ndipo anakhulupirira onse amene anaikidwiratu kumoyo wosatha.
Ndipo pamene anakwera kutuluka m'madzi, Mzimu wa Ambuye anakwatula Filipo; ndipo mdindo sanamuonenso, pakuti anapita njira yake wokondwera.