Machitidwe a Atumwi 7:21 - Buku Lopatulika ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa koma atamsiya pamtsinje paja, mwana wamkazi wa Farao adamtola, namlera ngati mwana wake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atakamutaya, mwana wamkazi wa Farao anamutola nakamulera ngati mwana wake. |
Ndi chikhulupiriro Mose, atakula msinkhu, anakana kutchedwa mwana wake wa mwana wamkazi wa Farao;