Machitidwe a Atumwi 7:18 - Buku Lopatulika kufikira inauka mfumu ina pa Ejipito, imene siinamdziwe Yosefe. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kufikira inauka mfumu ina pa Ejipito, imene siinamdziwa Yosefe. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pambuyo pake mfumu ina imene sidadziŵe Yosefe, idayamba kulamulira ku Ejipito. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pambuyo pake mfumu yatsopano imene sinkamudziwa Yosefe, inayamba kulamulira dziko la Igupto. |
Imeneyo inachenjerera fuko lathu, niwachitira choipa makolo athu, niwatayitsa tiana tao, kuti tingakhale ndi moyo.