Machitidwe a Atumwi 5:7 - Buku Lopatulika Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Patapita ngati maora atatu, mkazi wake adaloŵa, osadziŵa zimene zachitika. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Patapita maora atatu mkazi wake analowa, wosadziwa zimene zinachitika. |
Ndipo Petro ananena naye, Undiuze, ngati munagulitsa mundawo pa mtengo wakuti. Ndipo ananena, Inde, wakuti.