Machitidwe a Atumwi 3:3 - Buku Lopatulika ameneyo, pakuona Petro ndi Yohane akuti alowe mu Kachisi, anapempha alandire chaulere. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ameneyo, pakuona Petro ndi Yohane akuti alowe m'Kachisi, anapempha alandire chaulere. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene iye adaona Petro ndi Yohane akuloŵa m'Nyumba ya Mulungu, adaŵapempha kuti ampatseko kanthu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ataona Petro ndi Yohane ali pafupi kulowa anawapempha ndalama. |
Koma Petro ndi Yohane analikukwera kunka ku Kachisi pa ora lakupembedza, ndilo lachisanu ndi chinai.
Koma m'mene anagwira Petro ndi Yohane, anawathamangira pamodzi anthu onse kukhonde lotchedwa la Solomoni, alikudabwa ndithu.