Ndipo ine Daniele ndekha ndinaona masomphenyawo; pakuti anthu anali nane sanaone masomphenyawo; koma kunawagwera kunjenjemera kwakukulu, nathawa kubisala.
Machitidwe a Atumwi 22:9 - Buku Lopatulika Ndipo iwo akukhala nane anaonadi kuunika, koma sanamve mau akulankhula nane. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo iwo akukhala nane anaonadi kuunika, koma sanamva mau akulankhula nane. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anzanga apaulendo adaakuwona kuŵalako, koma mau a amene ankalankhula naneyo sadaŵamve. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Anzanga a paulendo anaona kuwalako, koma sanamve mawuwo, a Iye amene amayankhula nane. |
Ndipo ine Daniele ndekha ndinaona masomphenyawo; pakuti anthu anali nane sanaone masomphenyawo; koma kunawagwera kunjenjemera kwakukulu, nathawa kubisala.
dzuwa lamsana, ndinaona panjira, Mfumu, kuunika kochokera kumwamba kowalitsa koposa dzuwa kunawala pondizinga ine ndi iwo akundiperekeza.